Yohane 7:14, 15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chikondwererocho chitafika pakatikati, Yesu analowa mʼkachisi ndipo anayamba kuphunzitsa. 15 Ayudawo anadabwa nʼkufunsa kuti: “Kodi munthu ameneyu Malemba+ amenewa anawadziwa* bwanji, popeza sanapite kusukulu?”*+
14 Chikondwererocho chitafika pakatikati, Yesu analowa mʼkachisi ndipo anayamba kuphunzitsa. 15 Ayudawo anadabwa nʼkufunsa kuti: “Kodi munthu ameneyu Malemba+ amenewa anawadziwa* bwanji, popeza sanapite kusukulu?”*+