-
Machitidwe 5:27, 28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Choncho anabwera nawo nʼkuwaimika muholo ya Khoti Lalikulu la Ayuda. Ndipo mkulu wa ansembe ananena 28 kuti: “Tinakulamulani mwamphamvu kuti musaphunzitsenso mʼdzina limeneli.+ Koma mwadzaza Yerusalemu yense ndi mfundo zimene mukuphunzitsa ndipo mwatsimikiza mtima kuti ife tikhale ndi mlandu wa magazi a munthu ameneyu.”+
-