Machitidwe 3:9, 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu onse anamuona akuyenda ndi kutamanda Mulungu. 10 Iwo anamuzindikira kuti ndi munthu amene ankakhala pa Geti Lokongola la kachisi+ nʼkumapempha mphatso zachifundo. Ndipo anthuwo anadabwa kwambiri ndi zimene zinamuchitikirazo.
9 Anthu onse anamuona akuyenda ndi kutamanda Mulungu. 10 Iwo anamuzindikira kuti ndi munthu amene ankakhala pa Geti Lokongola la kachisi+ nʼkumapempha mphatso zachifundo. Ndipo anthuwo anadabwa kwambiri ndi zimene zinamuchitikirazo.