Machitidwe 5:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munthu wina, dzina lake Hananiya, ndi mkazi wake Safira, anagulitsa munda wawo. 2 Koma iye anachotsapo ndalama zina nʼkubisa ndipo mkazi wake anadziwa zimenezo. Ndiyeno anatenga ndalama zotsalazo nʼkukazipereka kwa atumwi.+
5 Munthu wina, dzina lake Hananiya, ndi mkazi wake Safira, anagulitsa munda wawo. 2 Koma iye anachotsapo ndalama zina nʼkubisa ndipo mkazi wake anadziwa zimenezo. Ndiyeno anatenga ndalama zotsalazo nʼkukazipereka kwa atumwi.+