-
Genesis 39:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Koma Yehova anali ndi Yosefe,+ moti chilichonse chimene ankachita chinkamuyendera bwino. Ndipo anaikidwa kuti aziyangʼanira nyumba ya munthu wa ku Iguputo uja, amene anali mbuye wake. 3 Mbuye wakeyo anaona kuti Yehova anali ndi mnyamatayo komanso kuti Yehova ankathandiza mnyamatayo kuti chilichonse chimene ankachita chiziyenda bwino.
-