Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mwana wamkazi wa Farao atapita kukasamba mumtsinje wa Nailo, atsikana ake omutumikira ankayenda mʼmphepete mwa mtsinjewo. Kenako iye anaona kabasiketi kaja kali pakati pa mabango. Nthawi yomweyo anatuma kapolo wake wamkazi kuti akakatenge.+

  • Ekisodo 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mwana uja atakula, anapita naye kwa mwana wa Farao, ndipo anakhala mwana wake.+ Zitatero anamʼpatsa dzina lakuti Mose* nʼkunena kuti: “Chifukwa chakuti ndinamuvuula mʼmadzi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena