Machitidwe 7:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Inu munalandira Chilamulo kudzera mwa angelo,+ koma osachitsatira.” Agalatiya 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiye nʼchifukwa chiyani Chilamulo chinaperekedwa? Anatipatsa Chilamulochi kuti machimo aonekere,+ mpaka mbadwa* imene inapatsidwa lonjezolo itafika.+ Angelo anapereka Chilamulocho+ kudzera mʼdzanja la mkhalapakati.+
19 Ndiye nʼchifukwa chiyani Chilamulo chinaperekedwa? Anatipatsa Chilamulochi kuti machimo aonekere,+ mpaka mbadwa* imene inapatsidwa lonjezolo itafika.+ Angelo anapereka Chilamulocho+ kudzera mʼdzanja la mkhalapakati.+