2 Mafumu 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anasiya malamulo onse a Yehova Mulungu wawo nʼkupanga zifaniziro ziwiri zachitsulo za ana a ngʼombe+ komanso mzati wopatulika.*+ Anayamba kugwadira gulu lonse la zinthu zakuthambo+ ndiponso kulambira Baala.+
16 Anasiya malamulo onse a Yehova Mulungu wawo nʼkupanga zifaniziro ziwiri zachitsulo za ana a ngʼombe+ komanso mzati wopatulika.*+ Anayamba kugwadira gulu lonse la zinthu zakuthambo+ ndiponso kulambira Baala.+