Deuteronomo 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dzanja la mbonizo lizikhala loyamba kumuponya miyala kuti afe, ndipo anthu ena onse azibwera pambuyo. Choncho muzichotsa woipayo pakati panu.+
7 Dzanja la mbonizo lizikhala loyamba kumuponya miyala kuti afe, ndipo anthu ena onse azibwera pambuyo. Choncho muzichotsa woipayo pakati panu.+