Salimo 69:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Msasa wawo* ukhale bwinja,Ndipo mʼmatenti awo musapezeke munthu wokhalamo.+