Mateyu 28:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho pitani mukaphunzitse anthu a mitundu yonse kuti akhale ophunzira anga.+ Muziwabatiza+ mʼdzina la Atate, la Mwana ndi la mzimu woyera, Machitidwe 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kirisipo,+ mtsogoleri wa sunagoge, anakhulupirira Ambuye pamodzi ndi anthu onse a mʼbanja lake. Ndipo anthu ambiri a ku Korinto, amene anamva uthenga wabwino, anayamba kukhulupirira nʼkubatizidwa.
19 Choncho pitani mukaphunzitse anthu a mitundu yonse kuti akhale ophunzira anga.+ Muziwabatiza+ mʼdzina la Atate, la Mwana ndi la mzimu woyera,
8 Kirisipo,+ mtsogoleri wa sunagoge, anakhulupirira Ambuye pamodzi ndi anthu onse a mʼbanja lake. Ndipo anthu ambiri a ku Korinto, amene anamva uthenga wabwino, anayamba kukhulupirira nʼkubatizidwa.