Machitidwe 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu onsewo anasangalala ndi mawu amenewa moti anasankha Sitefano, munthu wa chikhulupiriro cholimba ndiponso wodzaza ndi mzimu woyera. Anasankhanso Filipo,+ Purokoro, Nikanora, Timoni, Paremena ndi Nikolao wa ku Antiokeya amene analowa Chiyuda.
5 Anthu onsewo anasangalala ndi mawu amenewa moti anasankha Sitefano, munthu wa chikhulupiriro cholimba ndiponso wodzaza ndi mzimu woyera. Anasankhanso Filipo,+ Purokoro, Nikanora, Timoni, Paremena ndi Nikolao wa ku Antiokeya amene analowa Chiyuda.