1 Akorinto 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma pomaliza anaonekera kwa ine,+ ngati khanda lobadwa masiku osakwana.