-
Machitidwe 17:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Choncho mwachizolowezi chake,+ Paulo analowa mʼsunagogemo ndipo kwa milungu itatu anakambirana nawo mfundo za mʼMalemba.+ 3 Iye ankafotokoza ndiponso kusonyeza umboni wolembedwa powatsimikizira kuti zinali zoyenera kuti Khristu avutike,+ kenako auke.+ Ankanena kuti: “Yesu amene ndikumulalikira kwa inu, ndiye Khristu.”
-