2 Akorinto 11:32, 33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ku Damasiko, bwanamkubwa wa mfumu Areta anaika alonda mʼmageti a mzinda wa Damasiko kuti andigwire. 33 Koma anthu anandiika mʼdengu nʼkunditsitsira pawindo la mpanda wa mzindawo+ ndipo ndinapulumuka mʼmanja mwake.
32 Ku Damasiko, bwanamkubwa wa mfumu Areta anaika alonda mʼmageti a mzinda wa Damasiko kuti andigwire. 33 Koma anthu anandiika mʼdengu nʼkunditsitsira pawindo la mpanda wa mzindawo+ ndipo ndinapulumuka mʼmanja mwake.