Mateyu 28:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma mngeloyo anauza azimayiwo kuti: “Inu musachite mantha, chifukwa ndikudziwa kuti mukufuna Yesu amene anaphedwa popachikidwa pamtengo.+ 6 Muno mulibe chifukwa waukitsidwa mogwirizana ndi zimene ananena.+ Bwerani muone pamene anagona. Maliko 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anawauza kuti: “Musadabwe choncho.+ Ndikudziwa kuti mukufuna Yesu Mnazareti, amene anaphedwa popachikidwa pamtengo. Iyetu waukitsidwa kwa akufa,+ muno mulibe. Taonani, pamene anamugoneka paja si apa!+
5 Koma mngeloyo anauza azimayiwo kuti: “Inu musachite mantha, chifukwa ndikudziwa kuti mukufuna Yesu amene anaphedwa popachikidwa pamtengo.+ 6 Muno mulibe chifukwa waukitsidwa mogwirizana ndi zimene ananena.+ Bwerani muone pamene anagona.
6 Iye anawauza kuti: “Musadabwe choncho.+ Ndikudziwa kuti mukufuna Yesu Mnazareti, amene anaphedwa popachikidwa pamtengo. Iyetu waukitsidwa kwa akufa,+ muno mulibe. Taonani, pamene anamugoneka paja si apa!+