-
Luka 8:51Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
51 Atafika kunyumbako sanalole kuti aliyense alowe naye limodzi mʼnyumba kupatulapo Petulo, Yohane ndi Yakobo komanso bambo ndi mayi a mtsikanayo.
-