Luka 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Yesu anabwerera ku Galileya+ atadzazidwa ndi mphamvu ya mzimu. Ndipo mbiri yake yabwino inamveka paliponse mʼmadera onse ozungulira.
14 Tsopano Yesu anabwerera ku Galileya+ atadzazidwa ndi mphamvu ya mzimu. Ndipo mbiri yake yabwino inamveka paliponse mʼmadera onse ozungulira.