-
Luka 13:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Kodi sikunali koyenera kuti mayi uyu, amenenso ndi mwana wa Abulahamu, amene Satana anamumanga kwa zaka 18, amasulidwe mʼmaunyolo amenewa tsiku la Sabata?”
-