Luka 24:30, 31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamene ankadya nawo chakudya,* anatenga mkate nʼkuudalitsa, kenako anaunyemanyema nʼkuyamba kuwagawira.+ 31 Ataona zimenezi, maso awo anatsegukiratu ndipo anamuzindikira, koma iye anazimiririka.+ Yohane 21:13, 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yesu anapita kukatenga mkate nʼkuwagawira, ndipo anachitanso chimodzimodzi ndi nsomba. 14 Kameneka kanali kachitatu+ kuti Yesu aonekere kwa ophunzira akewo pambuyo poti waukitsidwa kwa akufa.
30 Pamene ankadya nawo chakudya,* anatenga mkate nʼkuudalitsa, kenako anaunyemanyema nʼkuyamba kuwagawira.+ 31 Ataona zimenezi, maso awo anatsegukiratu ndipo anamuzindikira, koma iye anazimiririka.+
13 Yesu anapita kukatenga mkate nʼkuwagawira, ndipo anachitanso chimodzimodzi ndi nsomba. 14 Kameneka kanali kachitatu+ kuti Yesu aonekere kwa ophunzira akewo pambuyo poti waukitsidwa kwa akufa.