10 Chifukwa aliyense wa ife adzaonekera kumpando woweruzira milandu wa Khristu, kuti alandire mphoto yake mogwirizana ndi zimene anachita ali mʼthupi, kaya zabwino kapena zoipa.+
4Pamaso pa Mulungu ndi Khristu Yesu, amene adzaweruze+ amoyo ndi akufa,+ akadzaonekera+ ndiponso akadzabwera mu Ufumu wake,+ ndikukulamula mwamphamvu kuti: