Machitidwe 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano onse anali atasonkhana pamodzi pa tsiku la Chikondwerero cha Pentekosite.+ Machitidwe 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno onsewo anadzazidwa ndi mzimu woyera+ ndipo anayamba kulankhula zilankhulo zosiyanasiyana,* mogwirizana ndi mmene mzimuwo unawachititsira kulankhula.+ Machitidwe 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Paulo atawagwira pamutu,* iwo analandira mzimu woyera+ ndipo anayamba kulankhula malilime* komanso kunenera.+
4 Ndiyeno onsewo anadzazidwa ndi mzimu woyera+ ndipo anayamba kulankhula zilankhulo zosiyanasiyana,* mogwirizana ndi mmene mzimuwo unawachititsira kulankhula.+
6 Ndiyeno Paulo atawagwira pamutu,* iwo analandira mzimu woyera+ ndipo anayamba kulankhula malilime* komanso kunenera.+