1 Petulo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Petulo mtumwi+ wa Yesu Khristu, ndikulembera inu osankhidwa ndi Mulungu, amene muli alendo mʼdzikoli, omwe mwamwazikana ku Ponto, Galatiya, Kapadokiya,+ Asia ndi Bituniya.
1 Ine Petulo mtumwi+ wa Yesu Khristu, ndikulembera inu osankhidwa ndi Mulungu, amene muli alendo mʼdzikoli, omwe mwamwazikana ku Ponto, Galatiya, Kapadokiya,+ Asia ndi Bituniya.