Machitidwe 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atafika mumzindawo anapita mʼchipinda chamʼmwamba, mmene ankakhala. Panali Petulo, Yohane, Yakobo, Andireya, Filipo, Tomasi, Batolomeyo, Mateyu, Yakobo mwana wa Alifeyo, Simoni wodzipereka uja komanso Yudasi mwana wa Yakobo.+
13 Atafika mumzindawo anapita mʼchipinda chamʼmwamba, mmene ankakhala. Panali Petulo, Yohane, Yakobo, Andireya, Filipo, Tomasi, Batolomeyo, Mateyu, Yakobo mwana wa Alifeyo, Simoni wodzipereka uja komanso Yudasi mwana wa Yakobo.+