Machitidwe 11:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Atamupeza anabwera naye ku Antiokeya. Iwo anasonkhana ndi mpingo kumeneko kwa chaka chathunthu ndipo anaphunzitsa anthu ambiri. Ku Antiokeya nʼkumene ophunzirawo anayamba kutchedwa Akhristu, motsogoleredwa ndi Mulungu.+
26 Atamupeza anabwera naye ku Antiokeya. Iwo anasonkhana ndi mpingo kumeneko kwa chaka chathunthu ndipo anaphunzitsa anthu ambiri. Ku Antiokeya nʼkumene ophunzirawo anayamba kutchedwa Akhristu, motsogoleredwa ndi Mulungu.+