Yohane 5:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Koma ine ndili ndi umboni woposa wa Yohane, chifukwa ntchito zimene Atate wanga anandipatsa kuti ndizikwaniritse, ntchito zimene ndikuchitazi, zikuchitira umboni kuti Atate ananditumadi.+ Yohane 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi sukukhulupirira kuti Atate ndi ine ndife ogwirizana?+ Zinthu zimene ndimakuuzani sindilankhula zamʼmaganizo mwanga,+ koma Atate amene ndi wogwirizana ndi ine ndi amene akuchita ntchito zake kudzera mwa ine.
36 Koma ine ndili ndi umboni woposa wa Yohane, chifukwa ntchito zimene Atate wanga anandipatsa kuti ndizikwaniritse, ntchito zimene ndikuchitazi, zikuchitira umboni kuti Atate ananditumadi.+
10 Kodi sukukhulupirira kuti Atate ndi ine ndife ogwirizana?+ Zinthu zimene ndimakuuzani sindilankhula zamʼmaganizo mwanga,+ koma Atate amene ndi wogwirizana ndi ine ndi amene akuchita ntchito zake kudzera mwa ine.