Machitidwe 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atakhala kumeneko kwa kanthawi, ananyamuka nʼkuyamba kuyenda malo osiyanasiyana mʼchigawo cha Galatiya ndi Fulugiya+ ndipo ankalimbikitsa ophunzira onse.+
23 Atakhala kumeneko kwa kanthawi, ananyamuka nʼkuyamba kuyenda malo osiyanasiyana mʼchigawo cha Galatiya ndi Fulugiya+ ndipo ankalimbikitsa ophunzira onse.+