Machitidwe 4:36, 37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho Yosefe, amene atumwiwo anamupatsa dzina lakuti Baranaba,+ kutanthauza “Mwana Wotonthoza,” amenenso anali Mlevi wobadwira ku Kupuro, 37 anali ndi munda. Iye anagulitsa mundawo nʼkubweretsa ndalamazo kudzazipereka kwa atumwi.+
36 Choncho Yosefe, amene atumwiwo anamupatsa dzina lakuti Baranaba,+ kutanthauza “Mwana Wotonthoza,” amenenso anali Mlevi wobadwira ku Kupuro, 37 anali ndi munda. Iye anagulitsa mundawo nʼkubweretsa ndalamazo kudzazipereka kwa atumwi.+