-
Machitidwe 19:24, 25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Panali munthu wina wosula siliva dzina lake Demetiriyo. Amisiri ankapindula kwambiri chifukwa cha ntchito yake yopanga tiakachisi tasiliva ta Atemi.+ 25 Demetiriyo anasonkhanitsa amisiriwo, limodzi ndi anthu ogwira ntchito yokhudza zinthu zimenezi. Ndiyeno anawauza kuti: “Anthu inu, mukudziwa kuti timapeza chuma kuchokera mu ntchito imeneyi.
-