Machitidwe 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako atumwi ndi akulu pamodzi ndi mpingo wonse, anagwirizana zosankha amuna pakati pawo, kuti awatumize ku Antiokeya limodzi ndi Paulo ndi Baranaba. Choncho anasankha Yudasi wotchedwa Barasaba ndi Sila,+ omwe ankatsogolera abale. Machitidwe 15:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Koma Paulo anasankha Sila, ndipo abale atamupempherera Pauloyo kuti Yehova* amusonyeze kukoma mtima kwakukulu, ananyamuka.+
22 Kenako atumwi ndi akulu pamodzi ndi mpingo wonse, anagwirizana zosankha amuna pakati pawo, kuti awatumize ku Antiokeya limodzi ndi Paulo ndi Baranaba. Choncho anasankha Yudasi wotchedwa Barasaba ndi Sila,+ omwe ankatsogolera abale.
40 Koma Paulo anasankha Sila, ndipo abale atamupempherera Pauloyo kuti Yehova* amusonyeze kukoma mtima kwakukulu, ananyamuka.+