Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 5:28, 29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Musadabwe nazo zimenezi, chifukwa nthawi ikubwera imene onse amene ali mʼmanda achikumbutso adzamva mawu ake+ 29 ndipo adzatuluka. Amene ankachita zabwino adzauka kuti alandire moyo ndipo amene ankachita zoipa adzauka kuti aweruzidwe.+

  • Yohane 11:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Yesu anamuuza kuti: “Ine ndine kuuka ndi moyo.+ Aliyense wokhulupirira ine, ngakhale atamwalira, adzakhalanso ndi moyo.

  • 1 Akorinto 15:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tsopano ngati timalalikira kuti Khristu anaukitsidwa,+ nʼchifukwa chiyani ena a inu akunena kuti akufa sadzaukitsidwa?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena