-
Machitidwe 23:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Kutacha, Ayuda anakonza chiwembu nʼkulumbira pochita kudzitemberera kuti saadya kapena kumwa chilichonse mpaka atapha Paulo.
-
-
Machitidwe 23:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Koma mwana wamwamuna wa mchemwali wake wa Paulo anamva kuti anthuwo akonza zokamudikirira panjira, ndipo anapita kumpanda wa asilikali nʼkukamuuza Paulo zimenezi.
-