Mateyu 26:27, 28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako anatenga kapu ya vinyo ndipo atayamika, anaipereka kwa iwo nʼkunena kuti: “Imwani nonsenu.+ 28 Vinyoyu akuimira ‘magazi anga+ a pangano,’+ amene adzakhetsedwe chifukwa cha anthu ambiri+ kuti machimo awo akhululukidwe.+ Aefeso 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kudzera mwa mwana wakeyu, tinamasulidwa ndi dipo* la magazi ake,+ inde, takhululukidwa machimo athu,+ mogwirizana ndi kukoma mtima kwake kwakukulu.
27 Kenako anatenga kapu ya vinyo ndipo atayamika, anaipereka kwa iwo nʼkunena kuti: “Imwani nonsenu.+ 28 Vinyoyu akuimira ‘magazi anga+ a pangano,’+ amene adzakhetsedwe chifukwa cha anthu ambiri+ kuti machimo awo akhululukidwe.+
7 Kudzera mwa mwana wakeyu, tinamasulidwa ndi dipo* la magazi ake,+ inde, takhululukidwa machimo athu,+ mogwirizana ndi kukoma mtima kwake kwakukulu.