Machitidwe 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma anthu ambiri amene anamvetsera mawu awo anakhulupirira, ndipo chiwerengero cha amuna chinakwana pafupifupi 5,000.+ Machitidwe 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso anthu okhulupirira Ambuye anapitiriza kuwonjezereka, chifukwa amuna ndi akazi ambirimbiri anakhala ophunzira.+
4 Koma anthu ambiri amene anamvetsera mawu awo anakhulupirira, ndipo chiwerengero cha amuna chinakwana pafupifupi 5,000.+
14 Komanso anthu okhulupirira Ambuye anapitiriza kuwonjezereka, chifukwa amuna ndi akazi ambirimbiri anakhala ophunzira.+