Machitidwe 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mogwirizana, onsewa ankalimbikira kupemphera pamodzi ndi Mariya mayi a Yesu, azimayi ena+ komanso azichimwene ake a Yesu.+
14 Mogwirizana, onsewa ankalimbikira kupemphera pamodzi ndi Mariya mayi a Yesu, azimayi ena+ komanso azichimwene ake a Yesu.+