Mateyu 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yesu anamuuza kuti: “Ngati ukufuna kukhala wangwiro,* pita ukagulitse katundu wako yense ndipo ndalama zake ukapatse osauka. Ukatero udzakhala ndi chuma kumwamba,+ ndiyeno ubwere udzakhale wotsatira wanga.”+
21 Yesu anamuuza kuti: “Ngati ukufuna kukhala wangwiro,* pita ukagulitse katundu wako yense ndipo ndalama zake ukapatse osauka. Ukatero udzakhala ndi chuma kumwamba,+ ndiyeno ubwere udzakhale wotsatira wanga.”+