Machitidwe 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Komanso, onse amene anakhulupirira anali ndi maganizo ofanana.* Panalibe aliyense amene ankanena kuti zinthu zimene anali nazo zinali zayekha. Zonse zimene anali nazo zinali za onse.+ Machitidwe 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndipotu panalibe aliyense amene ankasowa kanthu.+ Onse amene anali ndi minda kapena nyumba, ankagulitsa nʼkubweretsa ndalamazo.
32 Komanso, onse amene anakhulupirira anali ndi maganizo ofanana.* Panalibe aliyense amene ankanena kuti zinthu zimene anali nazo zinali zayekha. Zonse zimene anali nazo zinali za onse.+
34 Ndipotu panalibe aliyense amene ankasowa kanthu.+ Onse amene anali ndi minda kapena nyumba, ankagulitsa nʼkubweretsa ndalamazo.