-
Machitidwe 17:26, 27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Ndipo kuchokera mwa munthu mmodzi+ anapanga mitundu yonse ya anthu, kuti akhale padziko lonse lapansi.+ Iye anaika nthawi yoti zinthu zina zizichitika komanso anaika malire a malo oti anthu azikhala.+ 27 Anachita zimenezi kuti anthuwo afunefune Mulungu, amufufuzefufuze nʼkumupezadi,+ ngakhale kuti kwenikweni, iye sali kutali ndi aliyense wa ife.
-