Salimo 51:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Taonani! Ndinabadwa ndili wochimwa,Ndipo ndine wochimwa kuchokera pamene mayi anga anatenga pakati panga.+ Aroma 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Popeza anthu onse ndi ochimwa ndipo amalephera kusonyeza bwinobwino ulemerero wa Mulungu.+
5 Taonani! Ndinabadwa ndili wochimwa,Ndipo ndine wochimwa kuchokera pamene mayi anga anatenga pakati panga.+