Aroma 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yesu anaperekedwa chifukwa cha machimo athu+ ndipo anaukitsidwa kuti tionedwe olungama.+