1 Akorinto 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tonsefe tinabatizidwa ndi mzimu umodzi kuti tikhale thupi limodzi. Kaya ndife Ayuda kapena Agiriki, akapolo kapena anthu aufulu, tonsefe tinalandira* mzimu umodzi. Agalatiya 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chifukwa nonsenu amene munabatizidwa ndipo ndinu ogwirizana ndi Khristu mwakhala ndi makhalidwe ngati a Khristu.+
13 Tonsefe tinabatizidwa ndi mzimu umodzi kuti tikhale thupi limodzi. Kaya ndife Ayuda kapena Agiriki, akapolo kapena anthu aufulu, tonsefe tinalandira* mzimu umodzi.
27 Chifukwa nonsenu amene munabatizidwa ndipo ndinu ogwirizana ndi Khristu mwakhala ndi makhalidwe ngati a Khristu.+