Aheberi 9:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 nayenso Khristu anaperekedwa nsembe kamodzi kokha kuti anyamule machimo a anthu ambiri.+ Nthawi yachiwiri imene adzaonekere sadzaonekera nʼcholinga chochotsa uchimo. Ndipo amene adzamuone ndi anthu amene akumuyembekezera ndi mtima wonse kuti awapulumutse.+ 1 Petulo 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pajatu ngakhale Khristu anafa kamodzi kokha kuti achotse uchimo.+ Munthu wolungamayo anafera anthu osalungama+ kuti akugwirizanitseni ndi Mulungu.+ Iye anaphedwa monga munthu,*+ koma anaukitsidwa monga mzimu.+
28 nayenso Khristu anaperekedwa nsembe kamodzi kokha kuti anyamule machimo a anthu ambiri.+ Nthawi yachiwiri imene adzaonekere sadzaonekera nʼcholinga chochotsa uchimo. Ndipo amene adzamuone ndi anthu amene akumuyembekezera ndi mtima wonse kuti awapulumutse.+
18 Pajatu ngakhale Khristu anafa kamodzi kokha kuti achotse uchimo.+ Munthu wolungamayo anafera anthu osalungama+ kuti akugwirizanitseni ndi Mulungu.+ Iye anaphedwa monga munthu,*+ koma anaukitsidwa monga mzimu.+