Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Timoteyo 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Komabe, ndinachitiridwa chifundo kuti Khristu Yesu asonyeze kuleza mtima kwake konse kudzera mwa ine wochimwa kwambiri, kuti chikhale chitsanzo kwa amene adzamukhulupirire nʼcholinga choti adzapeze moyo wosatha.+

  • 1 Yohane 2:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ana anga okondedwa, ndikukulemberani zinthu izi kuti musachite tchimo. Komabe, wina akachita tchimo, tili ndi wotithandiza wolungama,+ Yesu Khristu,+ amene ali ndi Atate. 2 Iye anakhala nsembe yophimba+ machimo athu.*+ Osati athu okha, komanso a dziko lonse lapansi.+

  • Yuda 21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 kuti mupitirize kuchita zinthu zimene zingachititse kuti Mulungu azikukondani,+ pamene mukuyembekezera chifundo cha Ambuye wathu Yesu Khristu chomwe chidzachititse kuti mupeze moyo wosatha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena