Deuteronomo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo ndi mtundu winanso uti wamphamvu umene uli ndi malangizo komanso zigamulo zolungama zofanana ndi Chilamulo chonsechi chimene ndikukupatsani lero?+ Salimo 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Malamulo ochokera kwa Yehova ndi olungama, amasangalatsa mtima.+Chilamulo cha Yehova ndi choyera, chimatsegula maso.+
8 Ndipo ndi mtundu winanso uti wamphamvu umene uli ndi malangizo komanso zigamulo zolungama zofanana ndi Chilamulo chonsechi chimene ndikukupatsani lero?+
8 Malamulo ochokera kwa Yehova ndi olungama, amasangalatsa mtima.+Chilamulo cha Yehova ndi choyera, chimatsegula maso.+