Aroma 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kodi pa nthawiyo munkabala zipatso zotani? Zinali zinthu zimene panopa mumachita nazo manyazi. Ndipo mapeto a zinthu zimenezo ndi imfa.+
21 Kodi pa nthawiyo munkabala zipatso zotani? Zinali zinthu zimene panopa mumachita nazo manyazi. Ndipo mapeto a zinthu zimenezo ndi imfa.+