Afilipi 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zili choncho chifukwa inu munapatsidwa mwayi, osati wokhulupirira Khristu wokha, komanso wovutika chifukwa cha iye.+ Akolose 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano ndikusangalala ndi mavuto amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira monga chiwalo cha thupi la Khristu,+ limene ndi mpingo.+
29 Zili choncho chifukwa inu munapatsidwa mwayi, osati wokhulupirira Khristu wokha, komanso wovutika chifukwa cha iye.+
24 Tsopano ndikusangalala ndi mavuto amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira monga chiwalo cha thupi la Khristu,+ limene ndi mpingo.+