Yohane 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa Mulungu anakonda kwambiri dziko moti anapereka Mwana wake wobadwa yekha,+ kuti aliyense womukhulupirira asawonongedwe koma akhale ndi moyo wosatha.+ Aroma 3:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mulungu anamupereka ngati nsembe yoti anthu agwirizanenso ndi Mulunguyo+ pokhulupirira magazi ake.+ Anachita zimenezi pofuna kuonetsa chilungamo chake chifukwa anasonyeza kuti ndi wosakwiya msanga pokhululuka machimo amene anachitika kale. 1 Yohane 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zimene Mulungu anachita potisonyeza chikondi chake ndi izi: Anatumiza Mwana wake wobadwa yekha+ mʼdzikoli kuti tidzapeze moyo wosatha kudzera mwa iye.+
16 Chifukwa Mulungu anakonda kwambiri dziko moti anapereka Mwana wake wobadwa yekha,+ kuti aliyense womukhulupirira asawonongedwe koma akhale ndi moyo wosatha.+
25 Mulungu anamupereka ngati nsembe yoti anthu agwirizanenso ndi Mulunguyo+ pokhulupirira magazi ake.+ Anachita zimenezi pofuna kuonetsa chilungamo chake chifukwa anasonyeza kuti ndi wosakwiya msanga pokhululuka machimo amene anachitika kale.
9 Zimene Mulungu anachita potisonyeza chikondi chake ndi izi: Anatumiza Mwana wake wobadwa yekha+ mʼdzikoli kuti tidzapeze moyo wosatha kudzera mwa iye.+