2 Akorinto 4:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Timapanikizidwa mʼnjira zosiyanasiyana, koma osati mpaka kulephera kusuntha. Timathedwa nzeru, koma osati mpaka kusoweratu kothawira.*+ 9 Timazunzidwa, koma Mulungu samatisiya.+ Timagwetsedwa pansi, koma sitiwonongeka.+
8 Timapanikizidwa mʼnjira zosiyanasiyana, koma osati mpaka kulephera kusuntha. Timathedwa nzeru, koma osati mpaka kusoweratu kothawira.*+ 9 Timazunzidwa, koma Mulungu samatisiya.+ Timagwetsedwa pansi, koma sitiwonongeka.+