3 Ndikanakonda kuti ineyo ndisiyanitsidwe ndi Khristu ngati wotembereredwa mʼmalo mwa abale anga, anthu a mtundu wanga, 4 omwe ndi Aisiraeli. Mulungu anawatenga kuti akhale ana ake+ ndipo anawapatsa ulemerero, mapangano,+ Chilamulo,+ utumiki wopatulika+ komanso malonjezo.+