1 Akorinto 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngati ndikulalikira uthenga wabwino, chimenecho si chifukwa chodzitamira, chifukwa ndinalamulidwa kuchita zimenezi. Tsoka kwa ine ngati sindilalikira uthenga wabwino.+ 2 Akorinto 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ife tili ndi mtima wachikhulupiriro wofanana ndi zimene zinalembedwa kuti: “Ndinali ndi chikhulupiriro, choncho ndinalankhula.”+ Choncho ifenso tili ndi chikhulupiriro, ndipo tikulankhula, Aheberi 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu kudzera mwa Yesu.+ Kuchita zimenezi kuli ngati nsembe imene tikupereka kwa Mulungu ndipo timagwiritsa ntchito milomo yathu+ polengeza dzina lake.+
16 Ngati ndikulalikira uthenga wabwino, chimenecho si chifukwa chodzitamira, chifukwa ndinalamulidwa kuchita zimenezi. Tsoka kwa ine ngati sindilalikira uthenga wabwino.+
13 Ife tili ndi mtima wachikhulupiriro wofanana ndi zimene zinalembedwa kuti: “Ndinali ndi chikhulupiriro, choncho ndinalankhula.”+ Choncho ifenso tili ndi chikhulupiriro, ndipo tikulankhula,
15 Tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu kudzera mwa Yesu.+ Kuchita zimenezi kuli ngati nsembe imene tikupereka kwa Mulungu ndipo timagwiritsa ntchito milomo yathu+ polengeza dzina lake.+